1 Akorinto 4:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Ngakhale mutakhala ndi anthu okuyangʼanirani 10,000 mwa Khristu, mulibe abambo ambiri. Ine ndine bambo anu mwa Khristu Yesu chifukwa ndinakubweretserani uthenga wabwino.+ 1 Akorinto Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 4:15 Nsanja ya Olonda,8/1/1993, tsa. 15
15 Ngakhale mutakhala ndi anthu okuyangʼanirani 10,000 mwa Khristu, mulibe abambo ambiri. Ine ndine bambo anu mwa Khristu Yesu chifukwa ndinakubweretserani uthenga wabwino.+