Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Miyambo 10:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Miyambi ya Solomo.+

      Mwana wanzeru amakondweretsa bambo ake,+ koma mwana wopusa amamvetsa chisoni mayi ake.+

  • Miyambo 15:20
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 20 Mwana wanzeru ndi amene amakondweretsa bambo ake,+ koma wopusa amanyoza mayi ake.+

  • Miyambo 23:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 Mwana wanga, mtima wako ukakhala wanzeru,+ ndithu mtima wanga udzasangalala.+

  • Zefaniya 3:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 Yehova Mulungu wako ali pakati pa anthu ako ndipo adzakupulumutsa chifukwa ndi wamphamvu.+ Iye adzakondwera nawe.+ Adzakhala phee chifukwa chokhutira ndi chikondi chimene akukusonyeza, ndipo adzafuula mosangalala chifukwa chokondwera nawe.

  • 2 Yohane 4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Ndikusangalala kwambiri kuti ndapeza ena mwa ana+ anu akuyenda m’choonadi,+ mogwirizana ndi lamulo limene tinalandira kwa Atate.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena