Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Deuteronomo 30:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 Ndipo Yehova Mulungu wako adzakuchititsa kukhala ndi zinthu zosefukira pa ntchito iliyonse ya manja ako,+ chipatso cha mimba yako, chipatso cha ziweto zako+ ndi chipatso cha nthaka yako.+ Pamenepo udzatukuka+ chifukwa Yehova adzakondweranso nawe kuti akuchitire zabwino, monga mmene anakondwera ndi makolo ako.+

  • Salimo 147:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Yehova amasangalala ndi anthu amene amamuopa,+

      Amene amayembekezera kukoma mtima kwake kosatha.+

  • Yesaya 62:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Udzakhala chisoti chokongola m’dzanja la Yehova,+ ndiponso chisoti chachifumu m’dzanja la Mulungu wako.

  • Yesaya 65:19
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 19 Ndidzasangalala ndi Yerusalemu ndipo ndidzakondwera ndi anthu anga.+ Mwa iye simudzamvekanso kulira kokweza mawu kapena kulira kwachisoni.”+

  • Yeremiya 32:41
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 41 Ndidzakondwera nawo ndi kuwachitira zabwino.+ Ndidzawabzala m’dziko lino+ mokhulupirika ndi mtima wanga wonse komanso ndi moyo wanga wonse.’”

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena