Levitiko 26:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 ndidzakugwetserani mvula pa nthawi yake.+ Nthaka idzakupatsani chakudya,+ ndipo mitengo ya m’munda idzakupatsani zipatso zake.+ Salimo 67:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Dziko lapansi lidzapereka zipatso zake.+Mulungu, ndithu Mulungu wathu, adzatidalitsa.+ 2 Akorinto 9:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Tsopano amene amapereka mbewu kwa wobzala, amenenso amapereka chakudya kuti anthu adye,+ adzakupatsani mbewu zoti mubzale ndipo adzakupatsani zimenezi mowolowa manja. Adzawonjezeranso zipatso za chilungamo chanu.)+
4 ndidzakugwetserani mvula pa nthawi yake.+ Nthaka idzakupatsani chakudya,+ ndipo mitengo ya m’munda idzakupatsani zipatso zake.+
10 Tsopano amene amapereka mbewu kwa wobzala, amenenso amapereka chakudya kuti anthu adye,+ adzakupatsani mbewu zoti mubzale ndipo adzakupatsani zimenezi mowolowa manja. Adzawonjezeranso zipatso za chilungamo chanu.)+