Salimo 67:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Dziko lapansi lidzapereka zipatso zake.+Mulungu, ndithu Mulungu wathu, adzatidalitsa.+ Salimo 85:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Yehova nayenso adzapereka zinthu zabwino,+Ndipo dziko lathu lidzapereka zipatso zake.+ Zekariya 8:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 ‘M’dzikolo mudzakhala mbewu ya mtendere.+ Mpesa udzabala zipatso+ ndipo dziko lapansi lidzapereka zokolola zake.+ Kumwamba kudzagwetsa mame ake.+ Ndidzachititsa kuti anthu otsala+ mwa anthu awa adzalandire zinthu zonsezi.+
12 ‘M’dzikolo mudzakhala mbewu ya mtendere.+ Mpesa udzabala zipatso+ ndipo dziko lapansi lidzapereka zokolola zake.+ Kumwamba kudzagwetsa mame ake.+ Ndidzachititsa kuti anthu otsala+ mwa anthu awa adzalandire zinthu zonsezi.+