Mika 4:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Yehova wanena kuti, “Pa tsiku limenelo, ndidzasonkhanitsa anthu amene anali kuyenda motsimphina.+ Anthu amene anamwazikana ndidzawasonkhanitsa pamodzi.+ Ndidzasonkhanitsa pamodzi anthu amene ndawasautsa.
6 Yehova wanena kuti, “Pa tsiku limenelo, ndidzasonkhanitsa anthu amene anali kuyenda motsimphina.+ Anthu amene anamwazikana ndidzawasonkhanitsa pamodzi.+ Ndidzasonkhanitsa pamodzi anthu amene ndawasautsa.