Ezekieli 34:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 “Nkhosa zosochera ndidzazifunafuna,+ zomwazika ndidzazibweza. Yothyoka mwendo ndidzaimanga mwendo wothyokawo. Yodwala ndidzailimbitsa, koma yonenepa+ ndi yamphamvu ndidzaiwononga. Ndidzaipatsa chiweruzo monga chakudya chake.”+ Zefaniya 3:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Pa nthawi imeneyo ndidzaukira onse amene akukuzunza+ ndipo ndidzapulumutsa otsimphina.+ Anthu obalalitsidwa ndidzawasonkhanitsa pamodzi+ ndipo ndidzawachititsa kukhala otamandidwa komanso otchuka m’dziko lonse limene anachititsidwa manyazi. Aheberi 12:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Choncho limbitsani manja amene ali lende+ ndi mawondo olobodoka,+
16 “Nkhosa zosochera ndidzazifunafuna,+ zomwazika ndidzazibweza. Yothyoka mwendo ndidzaimanga mwendo wothyokawo. Yodwala ndidzailimbitsa, koma yonenepa+ ndi yamphamvu ndidzaiwononga. Ndidzaipatsa chiweruzo monga chakudya chake.”+
19 Pa nthawi imeneyo ndidzaukira onse amene akukuzunza+ ndipo ndidzapulumutsa otsimphina.+ Anthu obalalitsidwa ndidzawasonkhanitsa pamodzi+ ndipo ndidzawachititsa kukhala otamandidwa komanso otchuka m’dziko lonse limene anachititsidwa manyazi.