Yesaya 26:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Inu Yehova, dzanja lanu lakwezeka,+ koma iwo sakuliona.+ Iwo adzaona mmene mukudziperekera kwa anthu anu, ndipo adzachita manyazi.+ Ndithu, moto+ wanu udzanyeketsa adani anu. Yesaya 60:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 “Ana a anthu okusautsa adzabwera kwa iwe atawerama.+ Onse amene anali kukuchitira chipongwe adzagwada pamapazi ako,+ ndipo adzakutcha mzinda wa Yehova, Ziyoni+ wa Woyera wa Isiraeli. Zekariya 14:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 “Yehova adzapita kukamenyana ndi anthu a mitundu inawo+ ngati mmene anachitira pomenyana ndi adani ake m’mbuyomu.+
11 Inu Yehova, dzanja lanu lakwezeka,+ koma iwo sakuliona.+ Iwo adzaona mmene mukudziperekera kwa anthu anu, ndipo adzachita manyazi.+ Ndithu, moto+ wanu udzanyeketsa adani anu.
14 “Ana a anthu okusautsa adzabwera kwa iwe atawerama.+ Onse amene anali kukuchitira chipongwe adzagwada pamapazi ako,+ ndipo adzakutcha mzinda wa Yehova, Ziyoni+ wa Woyera wa Isiraeli.
3 “Yehova adzapita kukamenyana ndi anthu a mitundu inawo+ ngati mmene anachitira pomenyana ndi adani ake m’mbuyomu.+