Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yesaya 66:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 Pakuti ngati moto woyaka, Yehova adzaweruza anthu onse ndi lupanga lake,+ ndipo anthu ophedwa ndi Yehova adzakhala ambiri.+

  • Ezekieli 38:23
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 23 Ndidzadzilemekeza, kudziyeretsa+ ndi kuchititsa kuti mitundu yambiri ya anthu indidziwe, ndipo iwo adzadziwa kuti ine ndine Yehova.’+

  • Yoweli 3:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Makamu ambirimbiri a anthu ali m’chigwa+ choweruzira mlandu, pakuti tsiku la Yehova layandikira m’chigwa choweruzira mlandu.+

  • Chivumbulutso 16:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Kwenikweni amenewa ndi mauthenga ouziridwa+ ndi ziwanda ndipo amachita zizindikiro.+ Mauthengawo akupita kwa mafumu+ a dziko lonse lapansi+ kumene kuli anthu, kuti awasonkhanitsire pamodzi kunkhondo+ ya tsiku lalikulu+ la Mulungu Wamphamvuyonse.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena