Salimo 9:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Yehova amadziwika ndi ziweruzo zimene amapereka.+Woipa wakodwa mumsampha wa ntchito ya manja ake.+Higayoni.* [Seʹlah.] Ezekieli 25:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Anthu amenewa ndidzawalanga kwambiri ndi kuwadzudzula mwaukali,+ ndipo ndikadzawalanga adzadziwa kuti ine ndine Yehova.”’”+
16 Yehova amadziwika ndi ziweruzo zimene amapereka.+Woipa wakodwa mumsampha wa ntchito ya manja ake.+Higayoni.* [Seʹlah.]
17 Anthu amenewa ndidzawalanga kwambiri ndi kuwadzudzula mwaukali,+ ndipo ndikadzawalanga adzadziwa kuti ine ndine Yehova.”’”+