Salimo 86:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Ikani chizindikiro cha ubwino wanu pa ine,Kuti anthu odana nane aone zimenezi ndi kuchita manyazi,+Pakuti inu Yehova mwandithandiza ndi kundilimbikitsa.+ 1 Petulo 3:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Khalani ndi chikumbumtima chabwino,+ kuti ngakhale azikunenerani zoipa ndi kulankhula monyoza za khalidwe lanu labwino monga otsatira Khristu, adzachite manyazi.+ Chivumbulutso 3:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Taona! Anthu ochokera m’sunagoge wa Satana, amene amanama+ kuti ndi Ayuda+ pamene si Ayuda, ndidzawachititsa kuti abwere kudzagwada ndi kuwerama+ pamapazi ako. Ndipo ndidzawachititsa kudziwa kuti ndimakukonda.
17 Ikani chizindikiro cha ubwino wanu pa ine,Kuti anthu odana nane aone zimenezi ndi kuchita manyazi,+Pakuti inu Yehova mwandithandiza ndi kundilimbikitsa.+
16 Khalani ndi chikumbumtima chabwino,+ kuti ngakhale azikunenerani zoipa ndi kulankhula monyoza za khalidwe lanu labwino monga otsatira Khristu, adzachite manyazi.+
9 Taona! Anthu ochokera m’sunagoge wa Satana, amene amanama+ kuti ndi Ayuda+ pamene si Ayuda, ndidzawachititsa kuti abwere kudzagwada ndi kuwerama+ pamapazi ako. Ndipo ndidzawachititsa kudziwa kuti ndimakukonda.