Machitidwe 23:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Pamene anali kuyang’anitsitsa Khoti Lalikulu la Ayudalo, Paulo anati: “Amuna inu, abale anga, ndachita zinthu popanda chikumbumtima changa kunditsutsa ngakhale pang’ono pamaso pa Mulungu+ mpaka lero.” Machitidwe 24:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Pambali imeneyi, ndikuyesetsa mwakhama, kuchita mozindikira+ kuti ndisapalamule kwa Mulungu kapena kwa anthu. 1 Timoteyo 1:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Ndithu, cholinga chokulamulira zimenezi n’chakuti tikhale ndi chikondi+ chochokera mumtima woyera,+ m’chikumbumtima chabwino,+ ndiponso m’chikhulupiriro chopanda chinyengo.+ 1 Timoteyo 1:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Ukhale ndi chikhulupiriro ndi chikumbumtima chabwino+ chimene ena achikankhira kumbali,+ moti chikhulupiriro chawo chasweka ngati ngalawa.+ 1 Timoteyo 3:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Akhale ogwira chikhulupiriro mwamphamvu, chimene ndi chinsinsi chopatulika+ cha Mulungu, ali ndi chikumbumtima choyera.+
23 Pamene anali kuyang’anitsitsa Khoti Lalikulu la Ayudalo, Paulo anati: “Amuna inu, abale anga, ndachita zinthu popanda chikumbumtima changa kunditsutsa ngakhale pang’ono pamaso pa Mulungu+ mpaka lero.”
16 Pambali imeneyi, ndikuyesetsa mwakhama, kuchita mozindikira+ kuti ndisapalamule kwa Mulungu kapena kwa anthu.
5 Ndithu, cholinga chokulamulira zimenezi n’chakuti tikhale ndi chikondi+ chochokera mumtima woyera,+ m’chikumbumtima chabwino,+ ndiponso m’chikhulupiriro chopanda chinyengo.+
19 Ukhale ndi chikhulupiriro ndi chikumbumtima chabwino+ chimene ena achikankhira kumbali,+ moti chikhulupiriro chawo chasweka ngati ngalawa.+
9 Akhale ogwira chikhulupiriro mwamphamvu, chimene ndi chinsinsi chopatulika+ cha Mulungu, ali ndi chikumbumtima choyera.+