Mateyu 5:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 “Odala ndi anthu oyera mtima,+ chifukwa adzaona Mulungu.+ 2 Timoteyo 2:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Chotero, thawa zilakolako zaunyamata,+ koma tsatira chilungamo,+ chikhulupiriro, chikondi, ndi mtendere+ limodzi ndi anthu oitana pa Ambuye ndi mtima woyera.+
22 Chotero, thawa zilakolako zaunyamata,+ koma tsatira chilungamo,+ chikhulupiriro, chikondi, ndi mtendere+ limodzi ndi anthu oitana pa Ambuye ndi mtima woyera.+