1 Timoteyo 1:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Cholinga cha malangizo amenewa nʼchakuti tikhale ndi chikondi+ chochokera mumtima woyera, mʼchikumbumtima chabwino ndiponso mʼchikhulupiriro+ chopanda chinyengo. 1 Timoteyo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 1:5 Nsanja ya Olonda,9/15/2015, tsa. 9
5 Cholinga cha malangizo amenewa nʼchakuti tikhale ndi chikondi+ chochokera mumtima woyera, mʼchikumbumtima chabwino ndiponso mʼchikhulupiriro+ chopanda chinyengo.