1 Timoteyo 1:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Ndithu, cholinga chokulamulira zimenezi n’chakuti tikhale ndi chikondi+ chochokera mumtima woyera,+ m’chikumbumtima chabwino,+ ndiponso m’chikhulupiriro chopanda chinyengo.+ 1 Timoteyo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 1:5 Nsanja ya Olonda,9/15/2015, tsa. 9
5 Ndithu, cholinga chokulamulira zimenezi n’chakuti tikhale ndi chikondi+ chochokera mumtima woyera,+ m’chikumbumtima chabwino,+ ndiponso m’chikhulupiriro chopanda chinyengo.+