Machitidwe 23:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Pamene anali kuyang’anitsitsa Khoti Lalikulu la Ayudalo, Paulo anati: “Amuna inu, abale anga, ndachita zinthu popanda chikumbumtima changa kunditsutsa ngakhale pang’ono pamaso pa Mulungu+ mpaka lero.” Machitidwe 24:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Pambali imeneyi, ndikuyesetsa mwakhama, kuchita mozindikira+ kuti ndisapalamule kwa Mulungu kapena kwa anthu. 1 Timoteyo 3:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Akhale ogwira chikhulupiriro mwamphamvu, chimene ndi chinsinsi chopatulika+ cha Mulungu, ali ndi chikumbumtima choyera.+ 1 Petulo 3:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Khalani ndi chikumbumtima chabwino,+ kuti ngakhale azikunenerani zoipa ndi kulankhula monyoza za khalidwe lanu labwino monga otsatira Khristu, adzachite manyazi.+
23 Pamene anali kuyang’anitsitsa Khoti Lalikulu la Ayudalo, Paulo anati: “Amuna inu, abale anga, ndachita zinthu popanda chikumbumtima changa kunditsutsa ngakhale pang’ono pamaso pa Mulungu+ mpaka lero.”
16 Pambali imeneyi, ndikuyesetsa mwakhama, kuchita mozindikira+ kuti ndisapalamule kwa Mulungu kapena kwa anthu.
9 Akhale ogwira chikhulupiriro mwamphamvu, chimene ndi chinsinsi chopatulika+ cha Mulungu, ali ndi chikumbumtima choyera.+
16 Khalani ndi chikumbumtima chabwino,+ kuti ngakhale azikunenerani zoipa ndi kulankhula monyoza za khalidwe lanu labwino monga otsatira Khristu, adzachite manyazi.+