Aroma 12:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Musalole kuti choipa chikugonjetseni, koma pitirizani kugonjetsa choipa mwa kuchita chabwino.+ Tito 2:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Mawu ako akhale oyenera amene sangatsutsike,+ kuti munthu wotsutsa achite manyazi, ndipo asapeze choipa chotinenera nacho.+ 1 Petulo 2:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Khalani ndi khalidwe labwino pakati pa anthu a m’dzikoli,+ kuti pamene akukunenerani monga anthu ochita zoipa, pa mapeto pake iwo pokhala mboni zimene zikuona ndi maso zochita zanu zabwino,+ adzatamande Mulungu m’tsiku lake loyendera.+
8 Mawu ako akhale oyenera amene sangatsutsike,+ kuti munthu wotsutsa achite manyazi, ndipo asapeze choipa chotinenera nacho.+
12 Khalani ndi khalidwe labwino pakati pa anthu a m’dzikoli,+ kuti pamene akukunenerani monga anthu ochita zoipa, pa mapeto pake iwo pokhala mboni zimene zikuona ndi maso zochita zanu zabwino,+ adzatamande Mulungu m’tsiku lake loyendera.+