Mateyu 25:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Mitundu yonse ya anthu idzasonkhanitsidwa kwa iye+ ndipo adzalekanitsa+ anthu,+ mmene m’busa amalekanitsira nkhosa ndi mbuzi. Luka 19:44 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 44 Iwo adzakuwononga+ limodzi ndi ana ako amene ali mwa iwe. Ndipo sadzasiya mwala pamwala unzake+ mwa iwe, chifukwa sunazindikire kuti nthawi yokuyendera inali itakwana.”+ Machitidwe 17:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Chifukwa wakhazikitsa tsiku limene akufuna kudzaweruza+ m’chilungamo dziko lapansi kumene kuli anthu, kudzera mwa munthu amene iye wamuika. Ndipo wapereka chitsimikizo kwa anthu onse mwa kumuukitsa+ kwa akufa.”
32 Mitundu yonse ya anthu idzasonkhanitsidwa kwa iye+ ndipo adzalekanitsa+ anthu,+ mmene m’busa amalekanitsira nkhosa ndi mbuzi.
44 Iwo adzakuwononga+ limodzi ndi ana ako amene ali mwa iwe. Ndipo sadzasiya mwala pamwala unzake+ mwa iwe, chifukwa sunazindikire kuti nthawi yokuyendera inali itakwana.”+
31 Chifukwa wakhazikitsa tsiku limene akufuna kudzaweruza+ m’chilungamo dziko lapansi kumene kuli anthu, kudzera mwa munthu amene iye wamuika. Ndipo wapereka chitsimikizo kwa anthu onse mwa kumuukitsa+ kwa akufa.”