Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Hoseya 9:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 “Masiku oti uyenderedwe adzafika,+ masiku oti ulipire adzakwana+ ndipo anthu a Isiraeli adzadziwa zimenezi.+ Mneneri adzapusa+ ndipo munthu wolankhula mawu ouziridwa adzalusa, chifukwa cha kuchuluka kwa zolakwa zako+ ndiponso chifukwa cha kuchuluka kwa chidani.”

  • Mika 7:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Munthu wabwino kwambiri pakati pawo ali ngati chitsamba chaminga, ndipo munthu wowongoka mtima kwambiri pakati pawo ndi woipa kwambiri kuposa mpanda wa mitengo yaminga.+ Tsiku limene mudzapatsidwe chilango, limene alonda anu ananena, lidzafika ndithu.+ Pa tsikulo anthu adzathedwa nzeru.+

  • Luka 1:68
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 68 “Atamandike Yehova Mulungu wa Isiraeli,+ chifukwa wacheukira anthu ake+ ndi kuwapatsa chipulumutso.+

  • 1 Petulo 2:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Khalani ndi khalidwe labwino pakati pa anthu a m’dzikoli,+ kuti pamene akukunenerani monga anthu ochita zoipa, pa mapeto pake iwo pokhala mboni zimene zikuona ndi maso zochita zanu zabwino,+ adzatamande Mulungu m’tsiku lake loyendera.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena