Salimo 111:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Wawombola anthu ake.+ צ [Tsa·dhehʹ]Wakhazikitsa pangano lake mpaka kalekale.+ ק [Qohph]Dzina lake ndi loyera ndi lochititsa mantha.+ Luka 7:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Zitatero anthu onse anagwidwa ndi mantha,+ moti anayamba kutamanda Mulungu, kuti: “Mneneri wamkulu+ waonekera pakati pathu.” Analinso kunena kuti, “Mulungu wacheukira anthu ake.”+
9 Wawombola anthu ake.+ צ [Tsa·dhehʹ]Wakhazikitsa pangano lake mpaka kalekale.+ ק [Qohph]Dzina lake ndi loyera ndi lochititsa mantha.+
16 Zitatero anthu onse anagwidwa ndi mantha,+ moti anayamba kutamanda Mulungu, kuti: “Mneneri wamkulu+ waonekera pakati pathu.” Analinso kunena kuti, “Mulungu wacheukira anthu ake.”+