Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Deuteronomo 18:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 Yehova Mulungu wanu adzakupatsani mneneri ngati ine, kuchokera pakati panu, kuchokera pakati pa abale anu, ndipo inu mudzamvere mneneri ameneyo.+

  • Luka 24:19
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 19 Iye anawafunsa kuti: “Zinthu zotani?” Iwo anamuuza kuti: “Zinthu zokhudza Yesu Mnazareti,+ amene anali mneneri+ wamphamvu m’ntchito ndi m’mawu pamaso pa Mulungu ndi anthu onse.

  • Yohane 4:19
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 19 Mayiyo anati: “Bambo, ndazindikira kuti ndinu mneneri.+

  • Yohane 6:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Tsopano anthuwo ataona zizindikiro zimene anachitazo, anayamba kunena kuti: “Mosakayika uyu ndi mneneri+ uja amene anati adzabwera padziko.”

  • Yohane 7:40
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 40 Choncho ena m’khamulo, amene anamva mawu amenewa, anayamba kunena kuti: “Ameneyu ndi Mneneri ndithu.”+

  • Machitidwe 7:37
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 37 “Ameneyu ndi Mose amene anauza ana a Isiraeli kuti, ‘Mulungu adzakupatsani mneneri ngati ine, kuchokera pakati pa abale anu.’+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena