Luka 7:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Zitatero anthu onse anagwidwa ndi mantha,+ moti anayamba kutamanda Mulungu, kuti: “Mneneri wamkulu+ waonekera pakati pathu.” Analinso kunena kuti, “Mulungu wacheukira anthu ake.”+ Luka 7:39 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 39 Mfarisi amene anamuitana uja ataona izi, mumtima mwake anati: “Munthu uyu akanakhala mneneri,+ akanadziwa kuti mkazi amene akumugwirayu ndi ndani, ndiponso kuti ndi wotani. Akanadziwa kuti ndi wochimwa.”+ Yohane 9:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Ndiyeno Afarisiwo anafunsanso munthu amene anali wakhungu uja kuti: “Nanga iwe ukuti bwanji za munthu ameneyu, popeza kuti wakutsegula maso?” Munthuyo anati: “Ndi mneneri.”+
16 Zitatero anthu onse anagwidwa ndi mantha,+ moti anayamba kutamanda Mulungu, kuti: “Mneneri wamkulu+ waonekera pakati pathu.” Analinso kunena kuti, “Mulungu wacheukira anthu ake.”+
39 Mfarisi amene anamuitana uja ataona izi, mumtima mwake anati: “Munthu uyu akanakhala mneneri,+ akanadziwa kuti mkazi amene akumugwirayu ndi ndani, ndiponso kuti ndi wotani. Akanadziwa kuti ndi wochimwa.”+
17 Ndiyeno Afarisiwo anafunsanso munthu amene anali wakhungu uja kuti: “Nanga iwe ukuti bwanji za munthu ameneyu, popeza kuti wakutsegula maso?” Munthuyo anati: “Ndi mneneri.”+