Deuteronomo 18:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Mneneri akalankhula m’dzina la Yehova, koma mawuwo sanachitike kapena kukwaniritsidwa, ndiye kuti si Yehova amene walankhula mawu amenewo.+ Mneneriyo walankhula mawu amenewo mwa iye yekha, modzikuza. Iwe usachite naye mantha.’+ Yohane 4:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Mayiyo anati: “Bambo, ndazindikira kuti ndinu mneneri.+
22 Mneneri akalankhula m’dzina la Yehova, koma mawuwo sanachitike kapena kukwaniritsidwa, ndiye kuti si Yehova amene walankhula mawu amenewo.+ Mneneriyo walankhula mawu amenewo mwa iye yekha, modzikuza. Iwe usachite naye mantha.’+