Mateyu 2:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Atafika kumeneko anakakhala mumzinda wotchedwa Nazareti+ kuti akwaniritsidwe mawu onenedwa kudzera mwa aneneri kuti: “Iye adzatchedwa Mnazareti.”+ Mateyu 21:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Khamu la anthulo linali kuyankha kuti: “Ameneyu ndi mneneri+ Yesu, wochokera ku Nazareti, ku Galileya!”
23 Atafika kumeneko anakakhala mumzinda wotchedwa Nazareti+ kuti akwaniritsidwe mawu onenedwa kudzera mwa aneneri kuti: “Iye adzatchedwa Mnazareti.”+
11 Khamu la anthulo linali kuyankha kuti: “Ameneyu ndi mneneri+ Yesu, wochokera ku Nazareti, ku Galileya!”