Mateyu 21:46 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 46 Komabe, ngakhale kuti anali kufunafuna mpata wakuti amugwire, ankaopa khamu la anthu, chifukwa anthuwo anali kukhulupirira kuti iye ndi mneneri.+ Luka 7:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Zitatero anthu onse anagwidwa ndi mantha,+ moti anayamba kutamanda Mulungu, kuti: “Mneneri wamkulu+ waonekera pakati pathu.” Analinso kunena kuti, “Mulungu wacheukira anthu ake.”+ Luka 24:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Iye anawafunsa kuti: “Zinthu zotani?” Iwo anamuuza kuti: “Zinthu zokhudza Yesu Mnazareti,+ amene anali mneneri+ wamphamvu m’ntchito ndi m’mawu pamaso pa Mulungu ndi anthu onse.
46 Komabe, ngakhale kuti anali kufunafuna mpata wakuti amugwire, ankaopa khamu la anthu, chifukwa anthuwo anali kukhulupirira kuti iye ndi mneneri.+
16 Zitatero anthu onse anagwidwa ndi mantha,+ moti anayamba kutamanda Mulungu, kuti: “Mneneri wamkulu+ waonekera pakati pathu.” Analinso kunena kuti, “Mulungu wacheukira anthu ake.”+
19 Iye anawafunsa kuti: “Zinthu zotani?” Iwo anamuuza kuti: “Zinthu zokhudza Yesu Mnazareti,+ amene anali mneneri+ wamphamvu m’ntchito ndi m’mawu pamaso pa Mulungu ndi anthu onse.