Mateyu 21:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Khamu la anthulo linali kuyankha kuti: “Ameneyu ndi mneneri+ Yesu, wochokera ku Nazareti, ku Galileya!” Maliko 12:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Atamva zimenezo anayamba kufunafuna njira yomugwirira, koma anaopa khamu la anthu, pakuti iwo anazindikira kuti iye ananena fanizolo akuganiza za iwowo. Choncho anangomusiya n’kuchokapo.+ Yohane 7:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Afarisi anamva khamu la anthulo likunong’onezana motero za iye, ndipo ansembe aakulu ndi Afarisi anatuma alonda kuti akamugwire.+ Yohane 7:40 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 40 Choncho ena m’khamulo, amene anamva mawu amenewa, anayamba kunena kuti: “Ameneyu ndi Mneneri ndithu.”+
11 Khamu la anthulo linali kuyankha kuti: “Ameneyu ndi mneneri+ Yesu, wochokera ku Nazareti, ku Galileya!”
12 Atamva zimenezo anayamba kufunafuna njira yomugwirira, koma anaopa khamu la anthu, pakuti iwo anazindikira kuti iye ananena fanizolo akuganiza za iwowo. Choncho anangomusiya n’kuchokapo.+
32 Afarisi anamva khamu la anthulo likunong’onezana motero za iye, ndipo ansembe aakulu ndi Afarisi anatuma alonda kuti akamugwire.+
40 Choncho ena m’khamulo, amene anamva mawu amenewa, anayamba kunena kuti: “Ameneyu ndi Mneneri ndithu.”+