Mateyu 21:45 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 45 Tsopano ansembe aakulu ndi Afarisi atamvetsera mafanizo akewa, anazindikira kuti anali kunena za iwo.+ Maliko 11:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Ansembe aakulu ndi alembi anamva zimenezo, ndipo anayamba kufunafuna njira yomuphera,+ chifukwa anali kumuopa, pakuti khamu lonse la anthu nthawi zonse linali kudabwa ndi zimene anali kuphunzitsa.+ Luka 20:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Tsopano alembi ndi ansembe aakulu aja, pozindikira kuti iye anali kunena za iwo mufanizolo, anayesetsa kupeza mpata kuti amugwire ola lomwelo, koma anaopa anthu.+
45 Tsopano ansembe aakulu ndi Afarisi atamvetsera mafanizo akewa, anazindikira kuti anali kunena za iwo.+
18 Ansembe aakulu ndi alembi anamva zimenezo, ndipo anayamba kufunafuna njira yomuphera,+ chifukwa anali kumuopa, pakuti khamu lonse la anthu nthawi zonse linali kudabwa ndi zimene anali kuphunzitsa.+
19 Tsopano alembi ndi ansembe aakulu aja, pozindikira kuti iye anali kunena za iwo mufanizolo, anayesetsa kupeza mpata kuti amugwire ola lomwelo, koma anaopa anthu.+