Mateyu 21:46 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 46 Komabe, ngakhale kuti anali kufunafuna mpata wakuti amugwire, ankaopa khamu la anthu, chifukwa anthuwo anali kukhulupirira kuti iye ndi mneneri.+ Luka 19:48 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 48 Komabe anasowa chochita chifukwa anthu ambiri anali kungomuunjirira kuti amumvetsere ndipo sanali kusiyana naye.+
46 Komabe, ngakhale kuti anali kufunafuna mpata wakuti amugwire, ankaopa khamu la anthu, chifukwa anthuwo anali kukhulupirira kuti iye ndi mneneri.+
48 Komabe anasowa chochita chifukwa anthu ambiri anali kungomuunjirira kuti amumvetsere ndipo sanali kusiyana naye.+