Luka 19:48 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 48 Koma sanathe kuchita zimenezi chifukwa anthu ambiri ankangomuunjirira kuti amumvetsere ndipo sankasiyana naye.+ Luka Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 19:48 Yesu—Ndi Njira, tsa. 240 Nsanja ya Olonda,11/15/1989, tsa. 8
48 Koma sanathe kuchita zimenezi chifukwa anthu ambiri ankangomuunjirira kuti amumvetsere ndipo sankasiyana naye.+