Luka 19:48 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 48 Komabe anasowa chochita chifukwa anthu ambiri anali kungomuunjirira kuti amumvetsere ndipo sanali kusiyana naye.+ Luka Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 19:48 Yesu—Ndi Njira, tsa. 240 Nsanja ya Olonda,11/15/1989, tsa. 8
48 Komabe anasowa chochita chifukwa anthu ambiri anali kungomuunjirira kuti amumvetsere ndipo sanali kusiyana naye.+