Maliko 14:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Tsopano kunangotsala masiku awiri kuti pasika+ ndi chikondwerero+ cha mikate yopanda chofufumitsa zichitike.+ Ndipo ansembe aakulu ndi alembi anali kufunafuna njira yogwirira Yesu mochenjera ndi kumupha.+ Luka 19:47 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 47 Ndipo anali kuphunzitsa m’kachisimo tsiku ndi tsiku. Koma ansembe aakulu, alembi ndi akuluakulu a anthu anafunitsitsa kumupha.+ Luka 20:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Tsopano alembi ndi ansembe aakulu aja, pozindikira kuti iye anali kunena za iwo mufanizolo, anayesetsa kupeza mpata kuti amugwire ola lomwelo, koma anaopa anthu.+
14 Tsopano kunangotsala masiku awiri kuti pasika+ ndi chikondwerero+ cha mikate yopanda chofufumitsa zichitike.+ Ndipo ansembe aakulu ndi alembi anali kufunafuna njira yogwirira Yesu mochenjera ndi kumupha.+
47 Ndipo anali kuphunzitsa m’kachisimo tsiku ndi tsiku. Koma ansembe aakulu, alembi ndi akuluakulu a anthu anafunitsitsa kumupha.+
19 Tsopano alembi ndi ansembe aakulu aja, pozindikira kuti iye anali kunena za iwo mufanizolo, anayesetsa kupeza mpata kuti amugwire ola lomwelo, koma anaopa anthu.+