Maliko 11:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Ansembe aakulu ndi alembi anamva zimenezo, ndipo anayamba kufunafuna njira yomuphera,+ chifukwa anali kumuopa, pakuti khamu lonse la anthu nthawi zonse linali kudabwa ndi zimene anali kuphunzitsa.+ Yohane 7:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Mose anakupatsani Chilamulo,+ si choncho kodi? Komatu palibe ngakhale mmodzi wa inu amene amamvera Chilamulocho. Nanga n’chifukwa chiyani inu mukufuna kundipha?”+ Yohane 18:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Yesu anamuyankha kuti: “Ndalankhula poyera ku dzikoli. Nthawi zonse ndinali kuphunzitsa m’masunagoge ndi m’kachisi,+ kumene Ayuda onse anali kusonkhana, ndipo sindinalankhule kanthu mseri.
18 Ansembe aakulu ndi alembi anamva zimenezo, ndipo anayamba kufunafuna njira yomuphera,+ chifukwa anali kumuopa, pakuti khamu lonse la anthu nthawi zonse linali kudabwa ndi zimene anali kuphunzitsa.+
19 Mose anakupatsani Chilamulo,+ si choncho kodi? Komatu palibe ngakhale mmodzi wa inu amene amamvera Chilamulocho. Nanga n’chifukwa chiyani inu mukufuna kundipha?”+
20 Yesu anamuyankha kuti: “Ndalankhula poyera ku dzikoli. Nthawi zonse ndinali kuphunzitsa m’masunagoge ndi m’kachisi,+ kumene Ayuda onse anali kusonkhana, ndipo sindinalankhule kanthu mseri.