Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Mateyu 26:55
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 55 Mu ola lomwelo Yesu anafunsa khamu la anthulo kuti: “Bwanji mwabwera kudzandigwira mutatenga malupanga ndi zibonga ngati mukukalimbana ndi wachifwamba?+ Tsiku ndi tsiku ndinali kukhala pansi m’kachisi+ ndi kuphunzitsa, koma simunandigwire.

  • Luka 4:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 Komanso, anayamba kuphunzitsa m’masunagoge awo, ndipo anthu onse anali kumulemekeza.+

  • Luka 19:47
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 47 Ndipo anali kuphunzitsa m’kachisimo tsiku ndi tsiku. Koma ansembe aakulu, alembi ndi akuluakulu a anthu anafunitsitsa kumupha.+

  • Yohane 7:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Tsopano chikondwererocho chitafika pakatikati, Yesu analowa m’kachisi ndipo anayamba kuphunzitsa.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena