Luka 19:47 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 47 Ndipo anali kuphunzitsa m’kachisimo tsiku ndi tsiku. Koma ansembe aakulu, alembi ndi akuluakulu a anthu anafunitsitsa kumupha.+ Yohane 18:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Yesu anamuyankha kuti: “Ndalankhula poyera ku dzikoli. Nthawi zonse ndinali kuphunzitsa m’masunagoge ndi m’kachisi,+ kumene Ayuda onse anali kusonkhana, ndipo sindinalankhule kanthu mseri.
47 Ndipo anali kuphunzitsa m’kachisimo tsiku ndi tsiku. Koma ansembe aakulu, alembi ndi akuluakulu a anthu anafunitsitsa kumupha.+
20 Yesu anamuyankha kuti: “Ndalankhula poyera ku dzikoli. Nthawi zonse ndinali kuphunzitsa m’masunagoge ndi m’kachisi,+ kumene Ayuda onse anali kusonkhana, ndipo sindinalankhule kanthu mseri.