Luka 1:68 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 68 “Atamandike Yehova* Mulungu wa Isiraeli,+ chifukwa wakumbukira anthu ake nʼkuwabweretsera chipulumutso.+ 1. Kuwala Kwenikweni kwa Dziko Malifalensi a Mavidiyo a Uthenga Wabwino wa Yesu Ulosi wa Zekariya (gnj 1 27:15–30:56)
68 “Atamandike Yehova* Mulungu wa Isiraeli,+ chifukwa wakumbukira anthu ake nʼkuwabweretsera chipulumutso.+