Salimo 111:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Wawombola anthu ake.+ צ [Tsade] Walamula kuti pangano lake likhalepo mpaka kalekale. ק [Qoph] Dzina lake ndi loyera komanso lochititsa mantha.+ Luka 7:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Ataona zimenezi anthu onse anachita mantha ndipo anayamba kutamanda Mulungu kuti: “Mneneri wamkulu waonekera pakati pathu.”+ Ananenanso kuti, “Mulungu wakumbukira anthu ake.”+
9 Wawombola anthu ake.+ צ [Tsade] Walamula kuti pangano lake likhalepo mpaka kalekale. ק [Qoph] Dzina lake ndi loyera komanso lochititsa mantha.+
16 Ataona zimenezi anthu onse anachita mantha ndipo anayamba kutamanda Mulungu kuti: “Mneneri wamkulu waonekera pakati pathu.”+ Ananenanso kuti, “Mulungu wakumbukira anthu ake.”+