Ekisodo 15:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Munasonyeza chikondi chanu chokhulupirika potsogolera anthu amene munawawombola.+Ndi mphamvu zanu, mudzawatsogolera kudziko lanu lopatulika kumene mudzakhala. Luka 1:68 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 68 “Atamandike Yehova* Mulungu wa Isiraeli,+ chifukwa wakumbukira anthu ake nʼkuwabweretsera chipulumutso.+ Chivumbulutso 7:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Iwo anapitiriza kufuula ndi mawu okweza akuti: “Chipulumutso chathu chachokera kwa Mulungu wathu, amene wakhala pampando wachifumu,+ ndi kwa Mwanawankhosa.”+
13 Munasonyeza chikondi chanu chokhulupirika potsogolera anthu amene munawawombola.+Ndi mphamvu zanu, mudzawatsogolera kudziko lanu lopatulika kumene mudzakhala.
68 “Atamandike Yehova* Mulungu wa Isiraeli,+ chifukwa wakumbukira anthu ake nʼkuwabweretsera chipulumutso.+
10 Iwo anapitiriza kufuula ndi mawu okweza akuti: “Chipulumutso chathu chachokera kwa Mulungu wathu, amene wakhala pampando wachifumu,+ ndi kwa Mwanawankhosa.”+