1 Mafumu 1:48 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 48 Komanso mfumu inati, ‘Adalitsike+ Yehova Mulungu wa Isiraeli, amene lero wapereka munthu woti akhale pampando wanga wachifumu, ine ndikuona ndi maso anga.’”+ Salimo 41:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Adalitsike Yehova Mulungu wa Isiraeli,+Kuyambira kalekale mpaka kalekale.+Ame! Ame!*+ Salimo 72:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Adalitsike Yehova Mulungu, Mulungu wa Isiraeli,+Iye yekha amene akuchita ntchito zodabwitsa.+ Salimo 106:48 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 48 Adalitsike Yehova Mulungu wa Isiraeli,+Kuyambira kalekale mpaka kalekale.Ndipo anthu onse anene kuti, Ame.*+Tamandani Ya, anthu inu!+
48 Komanso mfumu inati, ‘Adalitsike+ Yehova Mulungu wa Isiraeli, amene lero wapereka munthu woti akhale pampando wanga wachifumu, ine ndikuona ndi maso anga.’”+
48 Adalitsike Yehova Mulungu wa Isiraeli,+Kuyambira kalekale mpaka kalekale.Ndipo anthu onse anene kuti, Ame.*+Tamandani Ya, anthu inu!+