1 Mbiri 16:36 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 36 Adalitsike Yehova Mulungu wa Isiraeli kuyambira kalekale mpaka kalekale.’”+Ndiyeno anthu onse ananena kuti, “Ame!”* n’kutamanda Yehova.+ Chivumbulutso 7:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Iwo anali kunena kuti: “Ame! Mulungu wathu wanzeru, wamphamvu+ ndi wa nyonga, atamandidwe, apatsidwe ulemerero ndi ulemu, ndipo ayamikiridwe kwamuyaya. Ame.”+
36 Adalitsike Yehova Mulungu wa Isiraeli kuyambira kalekale mpaka kalekale.’”+Ndiyeno anthu onse ananena kuti, “Ame!”* n’kutamanda Yehova.+
12 Iwo anali kunena kuti: “Ame! Mulungu wathu wanzeru, wamphamvu+ ndi wa nyonga, atamandidwe, apatsidwe ulemerero ndi ulemu, ndipo ayamikiridwe kwamuyaya. Ame.”+