Chivumbulutso 7:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Iwo ankanena kuti: “Ame! Mulungu wathu ndi amene ali ndi nzeru, mphamvu komanso nyonga ndipo ndi amene akuyenera kutamandidwa, kupatsidwa ulemerero ndi ulemu komanso kuyamikiridwa mpaka kalekale.+ Ame.” Chivumbulutso Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 7:12 Nsanja ya Olonda (Yophunzira),1/2021, tsa. 16 Mapeto a Chivumbulutso, tsa. 124
12 Iwo ankanena kuti: “Ame! Mulungu wathu ndi amene ali ndi nzeru, mphamvu komanso nyonga ndipo ndi amene akuyenera kutamandidwa, kupatsidwa ulemerero ndi ulemu komanso kuyamikiridwa mpaka kalekale.+ Ame.”