Chivumbulutso 7:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Iwo anali kunena kuti: “Ame! Mulungu wathu wanzeru, wamphamvu+ ndi wa nyonga, atamandidwe, apatsidwe ulemerero ndi ulemu, ndipo ayamikiridwe kwamuyaya. Ame.”+ Chivumbulutso Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 7:12 Nsanja ya Olonda (Yophunzira),1/2021, tsa. 16 Mapeto a Chivumbulutso, tsa. 124
12 Iwo anali kunena kuti: “Ame! Mulungu wathu wanzeru, wamphamvu+ ndi wa nyonga, atamandidwe, apatsidwe ulemerero ndi ulemu, ndipo ayamikiridwe kwamuyaya. Ame.”+