Chivumbulutso 4:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 “Ndinu woyenera, inu Yehova* Mulungu wathu kulandira ulemerero,+ ulemu+ ndi mphamvu+ chifukwa munalenga zinthu zonse+ ndipo mwa kufuna kwanu, zinakhalapo ndipo zinalengedwa.”
11 “Ndinu woyenera, inu Yehova* Mulungu wathu kulandira ulemerero,+ ulemu+ ndi mphamvu+ chifukwa munalenga zinthu zonse+ ndipo mwa kufuna kwanu, zinakhalapo ndipo zinalengedwa.”