Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Chivumbulutso 5:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Ndipo cholengedwa chilichonse chakumwamba, padziko lapansi, pansi pa nthaka,+ panyanja, ndi zinthu zonse zammenemo, ndinazimva zikunena kuti: “Mulungu amene wakhala pampando wachifumu+ komanso Mwanawankhosa,+ atamandidwe, alandire ulemu,+ ulemerero komanso mphamvu mpaka kalekale.”+

  • Chivumbulutso 7:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Iwo ankanena kuti: “Ame! Mulungu wathu ndi amene ali ndi nzeru, mphamvu komanso nyonga ndipo ndi amene akuyenera kutamandidwa, kupatsidwa ulemerero ndi ulemu komanso kuyamikiridwa mpaka kalekale.+ Ame.”

  • Chivumbulutso 11:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 Iwo ankanena kuti: “Tikukuthokozani inu Yehova,* Mulungu Wamphamvuyonse, inu amene mulipo+ ndi amene munalipo, chifukwa mwatenga mphamvu zanu zazikulu nʼkuyamba kulamulira monga mfumu.+

  • Chivumbulutso 12:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Ndinamva mawu ofuula kumwamba akuti:

      “Tsopano chipulumutso,+ mphamvu, Ufumu wa Mulungu wathu+ ndi ulamuliro wa Khristu wake zafika, chifukwa woneneza abale athu waponyedwa pansi. Iye amawaneneza masana ndi usiku pamaso pa Mulungu wathu.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena