Salimo 137:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Wodala ndi iye amene adzagwira ana ako ndi kuwaphwanya zidutswazidutswa+Mwa kuwawombetsa pathanthwe. Mika 3:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Chotero Ziyoni adzagawulidwa ngati munda chifukwa cha anthu inu ndipo Yerusalemu adzangokhala milu ya mabwinja.+ Phiri la nyumba ya Mulungu lidzakhala ngati zitunda za m’nkhalango. Luka 23:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Yesu anacheukira amayiwo ndi kunena kuti: “Ana aakazi a Yerusalemu inu, lekani kundilirira. Koma mudzilirire nokha ndi ana anu.+
9 Wodala ndi iye amene adzagwira ana ako ndi kuwaphwanya zidutswazidutswa+Mwa kuwawombetsa pathanthwe.
12 Chotero Ziyoni adzagawulidwa ngati munda chifukwa cha anthu inu ndipo Yerusalemu adzangokhala milu ya mabwinja.+ Phiri la nyumba ya Mulungu lidzakhala ngati zitunda za m’nkhalango.
28 Yesu anacheukira amayiwo ndi kunena kuti: “Ana aakazi a Yerusalemu inu, lekani kundilirira. Koma mudzilirire nokha ndi ana anu.+