Akolose 3:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Koma tsopano zonsezo muzitaye kutali ndi inu.+ Mutaye mkwiyo, kupsa mtima, kuipa, ndi mawu achipongwe,+ ndipo pakamwa panu pasatuluke nkhani zotukwana.+ 1 Timoteyo 6:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Ngati munthu akuphunzitsa chiphunzitso china,+ ndipo sakuvomereza mawu olondola,+ mawu a Ambuye wathu Yesu Khristu, ndiponso sakuvomereza chiphunzitso chogwirizana ndi kudzipereka kwathu kwa Mulungu,+
8 Koma tsopano zonsezo muzitaye kutali ndi inu.+ Mutaye mkwiyo, kupsa mtima, kuipa, ndi mawu achipongwe,+ ndipo pakamwa panu pasatuluke nkhani zotukwana.+
3 Ngati munthu akuphunzitsa chiphunzitso china,+ ndipo sakuvomereza mawu olondola,+ mawu a Ambuye wathu Yesu Khristu, ndiponso sakuvomereza chiphunzitso chogwirizana ndi kudzipereka kwathu kwa Mulungu,+