Aroma 2:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Pakuti iye amene ali Myuda kunja kokha si Myuda ayi,+ ndiponso mdulidwe wakunja kokha wochitidwa pathupi, si mdulidwe ayi.+ Chivumbulutso 2:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 ‘Ndikudziwa masautso ako ndi umphawi wako, koma ndiwe wolemera.+ Ndikudziwanso za kutonza kwa odzitcha Ayudawo,+ pamene si Ayuda, koma ndiwo sunagoge wa Satana.+
28 Pakuti iye amene ali Myuda kunja kokha si Myuda ayi,+ ndiponso mdulidwe wakunja kokha wochitidwa pathupi, si mdulidwe ayi.+
9 ‘Ndikudziwa masautso ako ndi umphawi wako, koma ndiwe wolemera.+ Ndikudziwanso za kutonza kwa odzitcha Ayudawo,+ pamene si Ayuda, koma ndiwo sunagoge wa Satana.+