Salimo 40:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 40 Ndinayembekezera Yehova ndi mtima wonse,+Choncho iye anatchera khutu kwa ine ndipo anamva kufuula kwanga kopempha thandizo.+ Salimo 71:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Kulitsani ulemu wanga,+Mundizungulire ndi chitetezo chanu ndi kundilimbikitsa.+
40 Ndinayembekezera Yehova ndi mtima wonse,+Choncho iye anatchera khutu kwa ine ndipo anamva kufuula kwanga kopempha thandizo.+