Salimo 71:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Anthu otsutsana nane achite manyazi, iwo awonongedwe.+Amene akufunafuna kundigwetsera tsoka adziphimbe ndi chitonzo ndiponso manyazi.+ Yesaya 41:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 “Taona! Onse okupsera mtima adzachita manyazi ndipo adzanyozeka.+ Anthu amene akukangana nawe sadzakhalanso ngati kanthu ndipo adzatha.+
13 Anthu otsutsana nane achite manyazi, iwo awonongedwe.+Amene akufunafuna kundigwetsera tsoka adziphimbe ndi chitonzo ndiponso manyazi.+
11 “Taona! Onse okupsera mtima adzachita manyazi ndipo adzanyozeka.+ Anthu amene akukangana nawe sadzakhalanso ngati kanthu ndipo adzatha.+