Ezekieli 34:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 “Nkhosa zosochera ndidzazifunafuna,+ zomwazika ndidzazibweza. Yothyoka mwendo ndidzaimanga mwendo wothyokawo. Yodwala ndidzailimbitsa, koma yonenepa+ ndi yamphamvu ndidzaiwononga. Ndidzaipatsa chiweruzo monga chakudya chake.”+ Mika 4:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Yehova wanena kuti, “Pa tsiku limenelo, ndidzasonkhanitsa anthu amene anali kuyenda motsimphina.+ Anthu amene anamwazikana ndidzawasonkhanitsa pamodzi.+ Ndidzasonkhanitsa pamodzi anthu amene ndawasautsa.
16 “Nkhosa zosochera ndidzazifunafuna,+ zomwazika ndidzazibweza. Yothyoka mwendo ndidzaimanga mwendo wothyokawo. Yodwala ndidzailimbitsa, koma yonenepa+ ndi yamphamvu ndidzaiwononga. Ndidzaipatsa chiweruzo monga chakudya chake.”+
6 Yehova wanena kuti, “Pa tsiku limenelo, ndidzasonkhanitsa anthu amene anali kuyenda motsimphina.+ Anthu amene anamwazikana ndidzawasonkhanitsa pamodzi.+ Ndidzasonkhanitsa pamodzi anthu amene ndawasautsa.