Zekariya 8:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 ‘Mʼdzikolo mudzadzalidwa mbewu ya mtendere. Mpesa udzabala zipatso ndipo dziko lapansi lidzatulutsa zokolola zake.+ Kumwamba kudzagwetsa mame ndipo ndidzachititsa kuti anthu otsala alandire zinthu zonsezi.+ Zekariya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 8:12 Nsanja ya Olonda,4/15/2006, ptsa. 26-271/1/1996, ptsa. 19-20
12 ‘Mʼdzikolo mudzadzalidwa mbewu ya mtendere. Mpesa udzabala zipatso ndipo dziko lapansi lidzatulutsa zokolola zake.+ Kumwamba kudzagwetsa mame ndipo ndidzachititsa kuti anthu otsala alandire zinthu zonsezi.+